Levitiko 18:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamacita monga mwa macitidwe a dziko la Aigupto muja munakhalamo; musamacita monga mwa macitidwe a dziko la Kanani kumene ndipita nanuko, nimusamayenda m'malemba ao.

Levitiko 18

Levitiko 18:1-5