Levitiko 17:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu ali yense wa ana a Israyeli, kapena mlendo wakugonera pakati pa inu, akasaka nyama kapena mbalame yakudya, nakaigwira; azikhetsa mwazi wace naufotsere ndi dothi.

Levitiko 17

Levitiko 17:11-15