Levitiko 15:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu ali yense wakukhudza kama wace azitsuka zobvala zace, nasambe m'madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo,

Levitiko 15

Levitiko 15:4-8