Levitiko 15:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu ali yense akakhudza zimenezi adzakhala wodetsedwa, natsuke zobvala zace, nasambe m'madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.

Levitiko 15

Levitiko 15:17-32