Levitiko 14:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo wansembe abviike cala cace ca dzanja lace lamanja ca iye mwini m'mafuta ali m'dzanja lace lamanzere, nawaze mafuta kasanu ndi kawiri ndi cala cace pamaso pa Yehova;

Levitiko 14

Levitiko 14:8-25