Levitiko 13:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma akaonapo wansembe, ndipo taonani, mulibe tsitsi loyera m'cikangamo, ndipo sicikumba kubzola khungu, koma cazimba; pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri;

Levitiko 13

Levitiko 13:25-28