Levitiko 13:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma wansembe akaciona, ndipo taonani, palibe tsitsi loyera pamenepo, ndipo sicinakumba kubzola khungu, koma cazimba, pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri;

Levitiko 13

Levitiko 13:15-29