Levitiko 13:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati khate libukabuka pakhungu, ndi khate lakuta khungu lonse la wanthendayo kuyambira mutu wace kufikira mapazi ace, monga momwe apenyera wansembe;

Levitiko 13

Levitiko 13:10-19