Levitiko 11:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ikafa nyama yakudya, iye amene akhudza mtembo wace adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.

Levitiko 11

Levitiko 11:29-42