Levitiko 10:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anati kwa Aroni, Ici ndi cimene Yehova ananena, ndi kuti, Mwa iwo akundiyandikiza ndipatulidwa Ine, ndi pamaso pa anthu onse ndilemekezedwa. Ndipo Aroni anakhala cete.

Levitiko 10

Levitiko 10:1-5