Levitiko 10:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapsa mtima pa Eleazara ndi Itamara, ana otsalawo a Aroni, nati, Mwalekeranji kudya nsembe yaucimo m'malo opatulika, pakuti ndiyo yopatulikitsa, ndipo iye anakupatsani iyo, kucotsera nayo mphulupulu ya khamulo, kuwacitira cowatetezera pamaso pa Yehova?

Levitiko 10

Levitiko 10:10-20