Levitiko 1:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wansembe abwere naco ku guwa la nsembe, namwetule mutu wace, naitenthe pa guwa la nsembe; ndi mwazi wace aukamulire pa mbali ya guwa la nsembe,

Levitiko 1

Levitiko 1:13-16