Hoseya 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti taonani, anacokera cionongeko, koma Aigupto adzawasonkhanitsa, Mofi adzawaika m'manda; khwisa adzalanda zofunika zao zasiliva; minga idzakhala m'mahema mwao.

Hoseya 9

Hoseya 9:3-7