Hoseya 9:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Coipa cao conse ciri m'Giligala; pakutipamenepo ndinawada, cifukwa ca kuipa kwa macitidwe ao ndidzawainga kuwacotsa m'nyumba mwanga; sindidzawakondanso; akalonga ao onse ndiwo opanduka.

Hoseya 9

Hoseya 9:9-17