Hoseya 7:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsoka kwa iwowa! pakuti anandizembera; cionongeko kwa iwowa! pakuti anandilakwira; ndikadawalanditsa Ine, koma anandinenera zabodza.

Hoseya 7

Hoseya 7:6-16