Hoseya 7:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzikuza kwa Israyeli kumcitira umboni pamaso pace; koma sanabwerera kumka kwa Yehova Mulungu wao, kapena kumfunafuna mwa ici conse.

Hoseya 7

Hoseya 7:1-14