Hoseya 5:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzamuka ndi kubwerera kumka kumalo kwanga, mpaka adzabvomereza kuparamula kwao, nafunafuna nkhope yanga; m'msauko mwao adzandifunafuna mwacangu.

Hoseya 5

Hoseya 5:13-15