Hoseya 2:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzadzibzalira iye m'nthaka, ndipo ndidzacitira cifundo Wosacitidwa-cifundo; ndipo ndidzati kwa Si-anthu-anga, Muli anthu anga; ndipo iwo adzati, Ndinu Mulungu wathu.

Hoseya 2

Hoseya 2:20-23