Hoseya 13:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzakomana nao ngati cimbalangondo cocilanda ana ace, ndi kung'amba cokuta mtima wao; ndi pomwepo ndidzawalusira ngati mkango; cirombo cidzawamwetula.

Hoseya 13

Hoseya 13:1-14