Hoseya 13:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Samariya adzasanduka wabwinja, pakuti anapandukana ndi Mulungu wace; iwo adzagwa ndi lupanga, ana ao amakanda adzaphwanyika, ndi akazi ao okhala ndi pakati adzatumbulidwa.

Hoseya 13

Hoseya 13:9-16