Hoseya 12:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Ine ndine Yehova Mulungu wako cicokere dziko la Aigupto, ndidzakukhalitsanso m'mahema, monga masiku a masonkhano oikika.

Hoseya 12

Hoseya 12:1-13