Hoseya 12:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova ali ndi mlandu ndi Yuda, nadzalanga Yakobo monga mwa njira zace, adzambwezera monga mwa macitidwe ace.

Hoseya 12

Hoseya 12:1-3