Hoseya 11:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sindidzacita mkwiyo wanga waukali, sindidzabwerera kuononga Efraimu; pakuti Ine ndine Mulungu, si munthu ai; Woyera wa pakati pako; ndipo sindidzalowa m'mudzi.

Hoseya 11

Hoseya 11:5-11