Hoseya 10:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mtima wao wagawikana, tsopano adzapezeka oparamula, adzapasula maguwa ao a nsembe, nadzaononga zoimiritsa zao.

Hoseya 10

Hoseya 10:1-5