Hoseya 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndidzacitira cifundo nyumba ya Yuda, ndi kuwapulumutsa mwa Ine Yehova Mulungu wao, osawapulumutsa ndi uta, kapena lupanga, kapena nkhondo ndi akavalo, kapena apakavalo.

Hoseya 1

Hoseya 1:1-11