Hoseya 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa iye, Umuche dzina lace Yezreeli; pakuti katsala kanthawi, ndipo ndidzabwezera cilango mwazi wa Yezreeli pa nyumba ya Yehu, ndi kuleketsa ufumu wa nyumba ya Israyeli.

Hoseya 1

Hoseya 1:3-9