Hoseya 1:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Yuda ndi ana a Israyeli adzasonkhanidwa pamodzi, nadzadziikira mkuru mmodzi, nadzakwera kucoka m'dziko; pakuti tsiku la Yezreeli ndi lalikuru.

Hoseya 1

Hoseya 1:1-11