Habakuku 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi Yehova anaipidwa nayo mitsinje?Mkwiyo wanu unali pamitsinje kodi,Kapena ukali wanu panyanja,Kuti munayenda pa akavalo anu,Pa magareta anu a cipulumutso?

Habakuku 3

Habakuku 3:1-17