Habakuku 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, moyo wace udzikuza, wosaongoka m'kati mwace; koma wolungama adzakhala ndi moyo mwa cikhulupiriro cace.

Habakuku 2

Habakuku 2:3-9