Habakuku 1:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akavalo ao aposa anyalugwe liwiro lao, aposa mimbulu ya madzulo ukali wao, ndipo apakavalo ao atanda; inde apakavalo ao afumira kutali; auluka ngati ciombankhanga cofulumira kudya.

Habakuku 1

Habakuku 1:1-10