Habakuku 1:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Si ndinu wacikhalire, Yehova Mulungu wanga, wopatulika wanga? sitidzafa. Yehova munamuikiratu kuti aweruzidwe; ndipo Inu, Thanthwe, munamkhazika kuti alangidwe.

Habakuku 1

Habakuku 1:6-17