Genesis 8:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo njiwa inadza kwa iye madzulo; ndipo, taonani, m'kamwa mwace munali tsamba lazitona lotyoledwa: ndipo anadziwa Nowa kuti madzi analimkuphwa pa dziko lapansi.

Genesis 8

Genesis 8:9-21