Genesis 7:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zinafa zamoyo zonse zoyenda pa dziko lapansi, zouluka, ndi nyama, ndi zamoyo, ndi zokwawa zonse zakukwawa pa dziko lapansi, ndi anthu onse:

Genesis 7

Genesis 7:17-24