Genesis 6:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaona Yehova kuti kuipa kwa anthu kunali kwakukuru pa dziko lapansi, ndiponso kuti ndingaliro zonse za maganizo a mitima yao zinali zoipabe zokhazokha.

Genesis 6

Genesis 6:1-8