Genesis 6:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati Yehova, Mzimu wanga sudzakangana ndi anthu nthawi zonse, cifukwa iwonso ndiwo thupi lanyama: koma masiku ace adzakhala zaka zana limodzi kudza makumi awiri.

Genesis 6

Genesis 6:1-9