Genesis 6:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zonse zokhala ndi moyo, ziwiri ziwiri za mtundu wao ulowetse m'cingalawamo, kuti zikhale ndi moyo pamodzi ndi iwe; zikhale zamphongo ndi zazikazi.

Genesis 6

Genesis 6:11-22