Genesis 6:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndine, taonani, ndipo Ine ndidzadzetsa cigumula ca madzi pa dziko lapansi, kuti cionooge zamoyo zonse, m'mene muli mpweya wa moyo pansi pa thambo; zinthu zonse za m'dziko lapansi zidzafa.

Genesis 6

Genesis 6:8-22