Genesis 6:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anati kwa Nowa, Cimariziro cace ca anthu onse cafika pamaso panga; pakuti dziko lapansi ladzala ndi ciwawa cifukwa ca iwo; taonani, ndidzaononga iwo pamodzi ndi dziko lapansi.

Genesis 6

Genesis 6:11-16