Genesis 50:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma inu, munandipangira ine coipa; koma Mulungu anacipangira cabwino, kuti kucitike monga lero, kupulumutsa amoyo anthu ambiri,

Genesis 50

Genesis 50:17-26