Genesis 5:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Metusela anakhala ndi moyo, atabala Lameke, zaka mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi atatu ndi ziwiri, nabala ana amuna ndi akazi:

Genesis 5

Genesis 5:25-29