Genesis 49:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Awa onse ndiwo mafuko khumi ndi awiri a Israyeli: izo ndizo zomwe ananena kwa iwo atate wao nawadalitsa; yense monga mdalitso wace anawadalitsa.

Genesis 49

Genesis 49:23-31