Genesis 48:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anati kwa atate wace, Amenewa ndi ana anga, amene Mulungu wandipatsa ine pano. Ndipo iye anati, Udze naotu kwa ine, ndipo ndidzawadalitsa.

Genesis 48

Genesis 48:7-11