Genesis 47:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma pamene ndidzagona ndi makolo anga, udzanditenge ine kuturuka m'dziko la Aigupto, ukandiike ine m'manda mwao. Ndipo iye anati, Ndidzacita monga mwanena.

Genesis 47

Genesis 47:24-31