Genesis 47:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anakhala m'dziko la Aigupto zaka khumi mphambu zisanu ndi ziwiri; ndipo masiku a Yakobo zaka za moyo wace zinali zaka zana limodzi mphambu makumi anai kudza zisanu ndi ziwiri.

Genesis 47

Genesis 47:26-31