Genesis 47:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anamgulira Farao dziko lonse la Aigupto, cifukwa Aaigupto anagulitsa yense munda wace, cifukwa njala inakula pa iwo; ndipo dziko linakhala la Farao.

Genesis 47

Genesis 47:16-24