Genesis 47:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anakhazika atate wace ndi abale ace, napatsa iwo pokhala m'dziko la Aigupto, m'dera lokometsetsa la m'dziko, m'dziko la Ramese, monga analamulira Farao.

Genesis 47

Genesis 47:6-20