Genesis 46:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anamanga gareta lace nakwera kunka kukakomana naye Israyeli atate wace, ku Goseni, ndipo anadzionetsera yekha kwa iye, nagwera pakhosi pace nakhala m'kulira pakhosi pace.

Genesis 46

Genesis 46:28-31