Genesis 46:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amenewa ndi ana a Biliha, amene Labani anampatsa Rakele mwana wace wamkazi, amenewo anambalira Yakobo; anthu onse ndiwo asanu ndi awiri.

Genesis 46

Genesis 46:20-32