Genesis 46:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amenewa ndi ana a Zilipa, amene Labani anampatsa Leya mwana wace wamkazi, amenewo anambalira Yakobo, anthu khumi ndi asanu ndi mmodzi.

Genesis 46

Genesis 46:14-21