Genesis 45:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano sindinu amene munanditumiza ine ndifike kuno, koma Mulungu, ndipo anandiyesa ine atate wa Farao, ndi mwini banja lace lonse, ndi wolamulira dziko lonse la Aigupto.

Genesis 45

Genesis 45:3-17